You're Genius Atupele. Osatopa Chilungamo chiziyenda Ngati Madzi. Ndi Mbuli yekha yomwe ingadane ndi inu. Koma yemwe Ali ndi nzeru Komaso Maso mphenya you're the only hope ya Malawi ❤️❤️ keep it up
Comfortable life killed his political dreams. I have no hopes in this young man..Burkina Faso, Senegal and France are lead by young men. Some successful and others not
Kodi sizingatheke anthu amene amaoneka ngati anzeru kut mwina akhonza kulamulira ndikubwera pamodzi posatengela political ambition like Atupele, kabambe Denis,kamangila and ena ambili amene amaonekeratu patali ngati pa tiktok you tube amene sindikwanisa kuwatchula koma mukawamvela inu aaaaaa mkumati awaso ndiye ndi mitu fuso mkumati sangabwere pamodzi?and when you look at them they are all young people